Wachiwiri kwa nduna ya za umoyo, Olemekezeka a Enock Phale lero akuyendera Chipatala cha Bwaila kuti amve okha zomwe zinachitika dzulo kuti ogwira ntchito wena afike polemba kuti tayamba kaye taimika ntchito zina pa chipatala maka zokhudza uchembere wabwino.
Tikupatsirane zonse pompano zomwe iwo anena.
